0.00 / 5 (0 user)
SKU: 11mun
Brand: No brand
MK1000.00

"Mundimve Yesu" Nyimbo yoyimbidwa ndi Evangelist Rhessah Mponda mu chaka cha 2016 kuchokera muchimbale chotchedwa "Mulungu wa zonse" yomwe ili yamu Khristumu nyimbo number 104.

"Mundimve Yesu" Nyimbo yoyimbidwa ndi Evangelist Rhessah Mponda mu chaka cha 2016 kuchokera muchimbale chotchedwa "Mulungu wa zonse" yomwe ili yamu Khristumu nyimbo number 104. Nyimboyi imakamba za munthu wochimwa amene akufuna kubwelela kwa Mulungu ndipo akupempha kupezekanso kwa Mulungu mmoyo mwake.