0.00 / 5 (0 user)
SKU: 3mul
Brand: No brand
MK1000.00

"Mulungu wa zonse" Nyimbo yoyimbidwa ndi Evangelist Rhessah Mponda mu chaka cha 2016 kuchokera muchimbale chotchedwa "Mulungu wa zonse."

"Mulungu wa zonse" Nyimbo yoyimbidwa ndi Evangelist Rhessah Mponda mu chaka cha 2016 kuchokera muchimbale chotchedwa "Mulungu wa zonse." Padziko lapansi pali milungu yambiri-mbiri yomwe anthu amayikhulupilila ndi kuyidalila. Ndipo milungu yambiri ili ndi zochita zowelengeka zokha, koma Yehovah ndi Mulungu wa zonse, Mulungu amene amatha kuchita china chilichonse chomwe ife tingasowe.